LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 January tsa. 2
  • January 1-7

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • January 1-7
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 January tsa. 2

January 1-7

MATEYU 1-3

  • Nyimbo 14 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Ufumu Wakumwamba Wayandikila”: (10 min.)

    • [Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Mateyu.]

    • Mat. 3:1, 2—Yohane M’batizi anali kulengeza kuti Mfumu ya m’tsogolo ya Ufumu wa kumwamba idzaonekela posacedwa (“Kulalikila,” “Ufumu,” “Ufumu wakumwamba,” “wayandikila” pa Mat. 3:1, 2 nwtsty mfundo zounikila)

    • Mat. 3:4—Yohane M’batizi anali na umoyo wosalila zambili, ndipo anali wodzipeleka kothelatu pocita cifunilo ca Mulungu. (“Covala ca Yohane M’batizi na Kaonekedwe Kake,” “Dzombe,” “Uci” zithunzi Mat. 3:4 nwtsty)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Mat. 1:3—M’buku la Mateyu, n’cifukwa ciani pa mzela wobadwila wa Yesu, wa amuna okha-okha, anaphatikizaponso azimayi asanu? (“Tamara” mfundo younikila pa Mat. 1:3 nwtsty)

    • Mat. 3:11—Tidziŵa bwanji kuti munthu pobatizika afunika kumila thupi lonse m’madzi? (“ndidzakubatizani” mfundo younikila pa Mat. 3:11 nwtsty)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mat. 1:1-17

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyo.

  • Ulendo Wobwelelako Woyamba: (3 min. olo kucepelelapo) Onani Makambilano a Citsanzo.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) bhs mape. 41-42 mapa. 6-7

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 72

  • Lipoti la Caka Cautumiki: (15 min.) Nkhani ya mkulu. Mukaŵelenga kalata yocokela ku ofesi ya nthambi yokamba za lipoti la caka cautumiki, funsani mafunso ofalitsa amene munawasankhilatu, amene anakhala na zocitika zabwino mu utumiki caka catha.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy Mutu 2

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 137 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani