LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 January tsa. 4
  • January 15-21

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • January 15-21
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 January tsa. 4

January 15-21

MATEYU 6-7

  • Nyimbo 21 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Pitilizani Kufuna-funa Ufumu Coyamba”: (10 min.)

    • Mat. 6:10—Ufumu unachulidwa pa zinthu zoyambilila m’pemphelo la citsanzo, kuonetsa kuti ni wofunika kwambili (bhs peji 178 pala. 12)

    • Mat. 6:24—Sitingathe kukhala kapolo wa Mulungu ndi wa “Cuma” (“kapolo” mfundo younikila Mat. 6:24 nwtsty)

    • Mat. 6:33—Yehova adzapeleka zosoŵa za atumiki ake okhulupilika oika zinthu za Ufumu patsogolo mu umoyo wawo (“pitilizani kufunafuna,” “Ufumu,” “cake,” “cilungamo” mfundo zounikila pa Mat. 6:33 nwtsty; w16.07 peji 12 pala. 18)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Mat. 7:12—Kodi vesiyi ingatithandize bwanji pokonzekela mau oyambila ulaliki? (w14 5/1 mape. 16, 17 mapa. 14-16)

    • Mat. 7:28, 29—Kodi khamu la anthu linakhudzidwa bwanji na zimene Yesu anali kuphunzitsa? Nanga n’cifukwa ciani? (“linadabwa,” “kaphunzitsidwe kake,” “osati monga alembi awo” mfundo zounikila pa Mat. 7:28, 29 nwtsty)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mat. 6:1-18

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano a citsanzo. Yankhani pa zimene ambili m’gawo lanu amakonda kukamba posafuna kulalikidwa.

  • Ulendo Wobwelelako Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano a citsanzo. Munthu amene munamulalikila mwapeza palibe, koma mwapezapo m’bululu wake.

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (5 min.) Tambani na kukambilana vidiyoyi.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 118

  • “Lekani Kuda Nkhawa”: (15 min.) Kukambilana. Yambani mwa kutambitsa vidiyo yakuti Zimene Tikuphunzilapo pa Mafanizo a Yesu—Onetsetsani Mbalame ndi Maluŵa.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 4

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 132 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani