LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 January tsa. 6
  • January 22-28

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • January 22-28
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 January tsa. 6

January 22-28

MATEYU 8-9

  • Nyimbo 17 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Yesu Anali Kukonda Anthu”: (10 min.)

    • Mat. 8:1-3—Yesu anaonetsa cifundo cacikulu kwa munthu wakhate (“n’kumukhudza,” “Ndikufuna” mfundo zounikila younikila pa Mat. 8:3,nwtsty)

    • Mat. 9:9-13—Yesu anali kukonda anthu ozondewa na ena (“kudya patebulo,” “okhometsa msonkho” mfundo zounikila pa Mat. 9:10, nwtsty)

    • Mat. 9:35-38—Kukonda anthu kunalimbikitsa Yesu kulalikila uthenga wabwino ngakhale pamene anali wolema. Analinso kupempha Mulungu kuti atumize anchito ambili (“anawamvela cisoni” mfundo younikila pa Mat. 9:36, nwtsty)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Mat. 8:8-10—Tingaphunzilepo ciani pa zimene Yesu anakambilana na kapitawo wa asilikali? (w02 8/15 peji 13 pala. 16)

    • Mat. 9:16, 17—Kodi Yesu anafuna kumveketsa mfundo yanji pa mafanizo aŵiliwa? (jy peji 70 pala. 6)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mat. 8:1-17

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano a citsanzo. Itanilani munthuyo ku misonkhano.

  • Ulendo Wobwelelako Wacitatu: (3 min. olo kucepelapo) Sankhani mwekha lemba na kugaŵila cofalitsa cophunzitsila Baibo.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) bhs mape. 46-47 mapa. 18-19

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 145

  • ‘Ndithu Mulungu Anamuika Kukhala Ambuye ndi Khristu’—Mbali 1, Kambali kake: (15 min.) Kukambilana. Mukaŵelenga Mateyu 9:18-25 na kutamba kavidiyo, kambilanani mafunso aya:

    • Kodi Yesu anacita ciani coonetsa kuti anaganizila mkazi wodwala ndiponso Yairo?

    • Kodi nkhani imeneyi imakhudza bwanji mmene mumaonela maulosi a m’Baibo okamba zimene Ufumu udzacita?

    • Tingaonetse m’njila ziti kuti timakonda anthu mmene Yesu anali kuwakondela?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 5

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 95 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani