LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 February tsa. 2
  • Mafanizo a Ufumu na Tanthauzo Lake Kwa Ise

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mafanizo a Ufumu na Tanthauzo Lake Kwa Ise
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Nkhani Zofanana
  • ‘Mvelani ndi Kumvetsa Tanthauzo Lake’
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2014
  • Mafanizo Ophunzitsadi Kanthu
    Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa
  • “Khulupililani Yehova Mulungu Wanu”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 February tsa. 2

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Mafanizo a Ufumu na Tanthauzo Lake Kwa Ise

Yesu anaseŵenzetsa mafanizo osavuta kumva pophunzitsa mfundo zozama za coonadi. Komabe, ni anthu odzicepetsa okha amene amamvetsetsa na kuseŵenzetsa zimene iye anaphunzitsa. (Mat. 13:10-15) Pa fanizo lililonse la Ufumu, yankhani mafunso otsatilawa: Kodi ningapindule bwanji na fanizoli? Nanga linganithandize bwanji mu umoyo wanga?

Kanjele ka mpilu, zofufumitsa, cuma, wamalonda woyendayenda

UFUMU WAKUMWAMBA ULI NGATI . . .

  • “kanjele ka mpilu.”—Mat. 13:31, 32. w14 12/15 peji 8 pala. 9.

  • “zofufumitsa.”—Mat. 13:33; w14 12/15 mape. 9-10 pala. 14-15.

  • “cuma” ndi “wamalonda woyendayenda.”—Mat. 13:44-46; w14 12/15 peji 10 pala. 18.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani