LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 April tsa. 5
  • April 23-29

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • April 23-29
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 April tsa. 5

April 23-29

MALIKO 3-4

  • Nyimbo 77 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Kucilitsa pa Sabata”: (10 min.)

    • Maliko 3:1, 2—Atsogoleli a cipembedzo aciyuda anali kufuna-funa pom’pezela cifukwa Yesu (jy peji 78 mapa. 1-2)

    • Maliko 3:3, 4—Yesu anadziŵa kuti anthuwo anali na maganizo olakwika kwambili osacokela m’malemba pa za lamulo la Sabata. (jy peji 78 pala. 3)

    • Maliko 3:5—Yesu anamva “cisoni kwambili cifukwa ca kuuma mtima kwawo.” (“mokwiya ndi kumva cisoni kwambili” nwtsty mfundo younikila)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Maliko 3:29—Kodi kunyoza mzimu woyela kumatanthauza ciani? Nanga kumabweletsa mavuto anji? (“wanyoza mzimu woyela,” “mlandu wa chimo losatha” nwtsty mfundo younikila)

    • Maliko 4:26-29—Kodi tingaphunzilepo ciani pa fanizo la Yesu la wofesa mbeu amene amagona? (w14 12/15 mape. 12-13 mapa. 6-8)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Maliko 3:1-19a

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Kubwelelako Kaciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.

  • Kubwelelako Kacitatu: (3 min. olo kucepelapo) Sankhani mwekha lemba na kugaŵila cofalitsa cophunzitsila Baibo.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) bhs peji 36 mapa. 21-22—Onetsani mmene mungamufikile pamtima.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 103

  • “Amene Ali ndi Makutu Akumva, Amve.”: (15 min.) Fotokozani zimene Maliko 4:9 itanthauza (nwtsty mfundo younikila). Tambitsani vidiyo yakuti Khalani Anzelu mwa Kulandila Uphungu. Ndiyeno, kambilanani zocokela m’buku la ‘Khalanibe M’cikondi ca Mulungu’ pa mapeji 46-47.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 18

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 123 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani