LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 April tsa. 6
  • April 30–May 6

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • April 30–May 6
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 April tsa. 6

April 30–May 6

MALIKO 5-6

  • Nyimbo 151 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Yesu Ali na Mphamvu Zokaukitsa Okondedwa Athu Amene Anamwalila”: (10 min.)

    • Maliko 5:38—Timalila ngati munthu amene timakonda wamwalila

    • Maliko 5:39-41—Yesu ali na mphamvu zokaukitsa anthu amene “akugona” mu imfa (“sanamwalile ayi, koma akugona” nwtsty mfundo younikila pa Maliko 5:39)

    • Maliko 5:42—Ciukililo cam’tsogolo cidzacititsa anthu ‘kusangalala kwambili’ (jy peji 118 pala. 6)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Maliko 5:19, 20—N’cifukwa ciani malangizo a Yesu panthawiyi anasiyana ndi a nthawi zonse? (“ukawauze” nwtsty mfundo younikila pa Maliko 5:19)

    • Maliko 6:11—Kodi ‘kusansa fumbi kumapazi’ kutanthauza ciani? (“sansani fumbi kumapazi anu” nwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Maliko 6:1-13

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Kubwelelako Kaciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Onetsani mwininyumba webusaiti yathu ya jw.org.

  • Kubwelelako Kacitatu: (3 min. olo kucepelapo) Dzisankhileni mwekha lemba, na funso lokakambilana pa ulendo wotsatila.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) bhs mape. 36 pala. 23-24—Onetsani mmene mungamufikile pa mtima.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 144

  • “Kuseŵenzetsa Mwaluso Zida Zophunzitsila za mu Thuboksi Yathu”: (5 min.) Kukambilana.

  • Kupeza Citonthozo m’Gulu la Yehova: (10 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi. Ndiyeno funsani mafunso aya: Kodi banja la m’bale Pera linakumana na mavuto anji? N’ciani cinawathandiza kupilila? N’cifukwa ciani tifunika kukhalabe okangalika mwauzimu pamene takumana na mavuto?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 19 mapa. 1-9

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 72 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani