LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 May tsa. 2
  • May 7-13

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • May 7-13
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 May tsa. 2

May 7-13

MALIKO 7–8

  • Nyimbo 13 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Nyamula Mtengo Wako Wozunzikilapo ndi Kunditsatila Mosalekeza”: (10 min.)

    • Maliko 8:34—Kuti titsatile Khristu, tifunika kudzikana tekha (“adzikane yekha” nwtsty mfundo younikila; w92 8/1 peji 17 pala. 14)

    • Maliko 8:35-37—Yesu anafunsa mafunso aŵili oticititsa kuganiza, amene angatithandize kuika maganizo athu pa zinthu zofunika kwambili (w08 10/15 mape. 25-26 mapa. 3-4)

    • Maliko 8:38—Kulimba mtima n’kofunika kuti titsatile Khristu (jy peji 143 pala. 4)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Maliko 7:5-8—N’cifukwa ciani kusamba m’manja kunali nkhani yaikulu kwa Afarisi? (w16.08 peji 30 mapa. 1-4)

    • Maliko 7:32-35—N’cifukwa ciani zimene Yesu anacita kwa munthu wogontha ni citsanzo cabwino kwa ise? (w00 2/15 mape. 17-18 mapa. 9-11)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Maliko 7:1-15

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Kubwelelako Koyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) bhs mape. 165-166 mapa. 6-7

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 51

  • Zofunikila za Mpingo: (5 min.)

  • “Thandizani Ana Anu Kuti Ayambe Kutsatila Khristu”: (10 min.) Kukambilana.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 19 mapa. 10-16, na bokosi pa peji. 50

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 60 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani