LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 June tsa. 4
  • June 11-17

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • June 11-17
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 June tsa. 4

June 11-17

LUKA 1

  • Nyimbo 137 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Tengelani Kudzicepetsa kwa Mariya”: (10 min.)

    • [Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Luka.]

    • Luka 1:38—Modzicepetsa, analandila nchito imene anapatsiwa (ia peji 149 pala. 12)

    • Luka 1:46-55—Anatamanda Yehova mwa kuchula Mau ake pokamba (ia mape. 150-151 mapa. 15-16)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Luka 1:69—Kodi mau akuti “nyanga yacipulumutso” atanthauza ciani? (“nyanga yacipulumutso” nwtsty mfundo younikila)

    • Luka 1:76—Kodi Yohane M’batizi ‘anatsogola pamaso pa Yehova’ m’lingalilo lanji? (“udzatsogola pamaso pa Yehova” nwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Luka 1:46-66

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.

  • Vidiyo ya Kubwelelako Koyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Kubwelelako Kaciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 92

  • Zofunikila za Mpingo: (8 min.) Ngati mufuna, kambilanani mfundo zokhudza lemba la caka ca 2018. (w18.01 mape. 8-9 mapa. 4-7)

  • Zimene Gulu Likukwanilitsa: (7 min.) Tambitsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Likukwanilitsa ya June.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 24

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 58 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani