LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 June tsa. 5
  • June 18-24

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • June 18-24
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 June tsa. 5

June 18-24

LUKA 2-3

  • Nyimbo 133 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Acicepele—Kodi Mukukula Mwauzimu?”: (10 min.)

    • Luka 2:41, 42—Yesu anapita ku cikondwelelo ca Pasika pamodzi na makolo ake (“makolo ake anali kukonda” nwtsty mfundo younikila pa Luka 2:41)

    • Luka 2:46, 47—Yesu anamvetsela kwa atsogoleli acipembedzo na kuwafunsa mafunso (“kuwafunsa mafunso,” “anadabwa kwambili” nwtsty mfundo zounikila)

    • Luka 2:51, 52—Yesu “anapitiliza kuwamvela” makolo ake, ndipo Mulungu komanso anthu anamukonda kwambili (“anapitiliza kuwamvela” nwtsty mfundo younikila)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Luka 2:14—Kodi vesiyi itanthauza ciani? (“ndipo pansi pano mtendele pakati pa anthu amene iye amakondwela nawo,” “anthu amene iye amakondwela nawo” nwtsty mfundo zounikila)

    • Luka 3:23—N’ndani anali tate wa Yosefe? (wp16.3 peji 9 mapa. 1-3)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Luka 2:1-20

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno, yankhani pa zimene anthu a m’gawo lanu amakamba posafuna kulalikidwa.

  • Vidiyo ya Kubwelelako Kaciŵili: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Nkhani: (6 min. olo kucepelapo) w14 2/15 mapeji 26-27—Mutu: N’chifukwa Chiyani Ayuda a M’nthawi ya Yohane M’batizi “Anali Kuyembekezera” Mesiya?

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 134

  • “Makolo, Thandizani Ana Anu Kuti Apambane”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Sanalekelele Mwayi Uliwonse wa Utumiki.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 25

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 17 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani