LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 July tsa. 5
  • July 23-29

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • July 23-29
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 July tsa. 5

July 23-29

LUKA 12-13

  • Nyimbo 4 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Ndinu Ofunika Kwambili Kuposa Mpheta Zambili”: (10 min.)

    • Luka 12:6—Ngakhale mbalame zing’ono-zing’ono Mulungu saziiŵala (“mpheta” nwtsty mfundo younikila)

    • Luka 12:7—Yehova amatidziŵa bwino kwambili. Uwu ni umboni wakuti amatikonda ngako (“ngakhale tsitsi lonse la m’mutu mwanu analiŵelenga” nwtsty mfundo younikila)

    • Luka 12:7—Yehova amaona aliyense wa ise kukhala wofunika (cl peji 241 mapa. 4-5)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Luka 13:24—Kodi zimene Yesu anakamba pa lembali zitanthauza ciani? (“Yesetsani mwamphamvu” nwtsty mfundo younikila)

    • Luka 13:33—N’cifukwa ciani Yesu anakamba mau amenewa? (“n’kosayenela” nwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Luka 12:22-40

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Kubwelelako Kaciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno itanilani mwininyumba ku misonkhano.

  • Kubwelelako Kacitatu: (3 min. olo kucepelapo) Sankhani mwekha lemba, ndipo gaŵilani cofalitsa cophunzitsila Baibo.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) lv mape. 184-185 mapa. 4-5

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 116

  • Sayenda Koma Sanaiŵalidwe: (15 min.) Tambitsani vidiyoyi. Pambuyo pake, kambilanani mafunso aya:

    • Kodi ofalitsa atatuwa anakumana na mavuto anji?

    • Kodi Yehova anawaonetsa bwanji kuti sanawaiŵale?

    • Kodi ofalitsawo anapitiliza bwanji kutumikila Yehova ngakhale kuti anakumana na mavuto? Nanga kucita zimenezi kunawalimbikitsa bwanji ofalitsa ena?

    • Kodi okalamba kapena odwala amene ali mu mpingo wanu mungawaonetse bwanji cikondi?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy Mutu 30

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 5 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2026)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani