LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 August tsa. 2
  • August 6-12

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • August 6-12
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 August tsa. 2

August 6-12

LUKA 17-18

  • Nyimbo 18 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Muzionetsa Kuyamikila”: (10 min.)

    • Luka 17:11-14—Yesu anacilitsa anthu 10 akhate (“amuna 10 akhate” nwtsty mfundo zounikila pa Luka 17:12, 14 “mukadzionetse kwa ansembe”)

    • Luka 17:15, 16—Wakhate mmodzi cabe ndiye anabwelela kukayamikila Yesu

    • Luka 17:17, 18—Nkhani imeneyi itiunikila kufunika koonetsa kuyamikila (w08 8/1 mape. 14-15 mapa. 8-9)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Luka 17:7-10—Kodi mfundo ya Yesu m’fanizo ili ni yotani? (“opanda pake” nwtsty mfundo younikila pa Luka 17:10)

    • Luka 18:8—Ni cikhulupililo cotani cimene Yesu anali kutanthauza pa vesiyi? (“cikhulupililo” nwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Luka 18:24-43

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Kubwelelako Koyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) fg phunzilo 4 mapa. 1-2

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 39

  • “Kumbukilani Mkazi wa Loti”: (15 min.) Kukambilana.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 32

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 117 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani