LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 August tsa. 5
  • August 20-26

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • August 20-26
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 August tsa. 5

August 20-26

LUKA 21-22

  • Nyimbo 27 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Cipulumutso Canu Cikuyandikila”: (10 min.)

    • Luka 21:25—Pa cisautso cacikulu padzacitika zinthu zocititsa mantha (kr peji 226 pala. 9)

    • Luka 21:26—Adani a Yehova adzacita mantha

    • Luka 21:27, 28—Kubwela kwa Yesu kudzatanthauza cipulumutso kwa anthu okhulupilika (w16.01 mape 10-11 pala. 17; w15 7/15 mape 17-18 pala. 13)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Luka 21:33—Kodi zimene Yesu anakamba pa vesiyi zitanthauza ciani? (“Kumwamba ndi dziko lapansi zidzacoka,” “mau anga sadzacoka ayi” nwtsty mfundo zounikila)

    • Luka 22:28-30—Kodi Yesu anacita pangano lanji, nanga anacita na ndani? Kodi panganolo lidzatheketsa ciani? (w14 10/15 mape 16-17 mapa. 15-16)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Luka 22:35-53

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Onetsani mmene mungayankhile pa zimene anthu a m’gawo lanu amakamba posafuna kulalikidwa.

  • Kubwelelako Koyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na akambilano acitsanzo. Onetsani mmene mungacitile ngati mwininyumba ni wotangwanika.

  • Vidiyo ya Kubwelelako Kaciŵili: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 136

  • Zofunikila za Mpingo: (15 min.)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 34

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 41 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani