LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 October tsa. 3
  • October 8-14

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • October 8-14
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 October tsa. 3

October 8-14

YOHANE 11-12

  • Nyimbo 16 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Tengelani Cifundo ca Yesu”: (10 min.)

    • Yoh. 11:23-26—Yesu anakamba mawu otonthoza kwa Marita (“Ndikudziŵa kuti adzauka” nwtsty mfundo zounikila pa Yoh. 11:24, “Ine ndine kuuka ndi moyo” 25)

    • Yoh. 11:33-35—Yesu anamva cisoni cacikulu ataona Mariya na anthu ena akulila (“Kulila,” “anadzuma . . . ndi kumva cisoni,” “mu mtima” “kugwetsa misozi” nwtsty mfundo zounikila)

    • Yoh. 11:43, 44—Yesu anacitapo kanthu kuti athandize anthu

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Yoh. 11:49—N’ndani anaika Kayafa kuti akhale mkulu wa ansembe? Nanga anakhala mkulu wa ansembe kwa nthawi yaitali bwanji? (“mkulu wa ansembe” nwtsty mfundo younikila)

    • Yoh. 12:42—N’cifukwa ciani Ayuda ena anacita mantha kuvomeleza poyela kuti Yesu ni Khristu? (“olamulila,” “angawacotse musunagoge” nwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Yoh. 12:35-50

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.

  • Vidiyo ya Kubwelelako Koyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Nkhani: (6 min. olo kucepelapo ) w13 9/15 peji 32—Mutu: N’cifukwa Ciani Yesu Anagwetsa Misozi Asanaukitse Lazaro?

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 141

  • Yesu Ndiye “Kuuka ndi Moyo” (Yoh. 11:25): (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti ‘Ndithu Mulungu Anamuika Kukhala Ambuye ndi Khristu’—Mbali 2, Kambali Kake. Ndiyeno funsani omvela mafunso otsatilawa: Kodi nkhaniyi itiphunzitsa ciani za cifundo ca Yesu? Kodi Yesu ni “kuuka ndi moyo” m’njila iti? Ni zozizwitsa zotani zimene Yesu adzacita m’tsogolo?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu. 38

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 147 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani