LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 October tsa. 4
  • October 15-21

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • October 15-21
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 October tsa. 4

October 15-21

YOHANE 13-14

  • Nyimbo 100 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Ndakupatsani Citsanzo”: (10 min.)

    • Yoh. 13:5—Yesu anasambika mapazi a ophunzila ake (“kusambitsa mapazi a ophunzila” nwtsty mfundo younikila)

    • Yoh. 13:12-14—Ophunzila ake ndiwo anali na udindo ‘wosambikana mapazi’ (“muyenela” nwtsty mfundo younikila)

    • Yoh. 13:15—Ophunzila onse a Yesu afunika kutengela citsanzo cake ca kudzicepetsa (w99 3/1 peji 31 pala. 1)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Yoh. 14:6—Kodi Yesu ni “njila, coonadi ndi moyo” m’lingalilo lanji? (“Ine ndine njila, coonadi ndi moyo” nwtsty mfundo younikila)

    • Yoh. 14:12—Kodi amene amakhulupilila mwa Yesu ‘amacita nchito zazikulu kuposa’ zake motani? (“nchito zazikulu kuposa zimenezi” nwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Yoh. 13:1-17

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo pamene mucita ulaliki wamwayi.

  • Kubwelelako Koyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.

  • Vidiyo ya Kubwelelako Kaciŵili: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 114

  • “Akhristu Oona Amadziŵika na Cikondi—Pewani Kunyada ndi Kucita Zosayenela”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti “Muzikondana”—Pewani Kunyada ndi Kucita Zosayenela. Ngati nthawi ilola, kambilanani kabokosi kakuti “Citsanzo ca m’Baibo Cofunika Kucisinkha-sinkha.”

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu. 39

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 120 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani