November 5-11
YOHANE 20-21
Nyimbo 35 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Umandikonda Ine Kuposa Izi?”: (10 min.)
Yoh. 21:1-3—Pambuyo pa imfa ya Yesu, Petulo na ophunzila ena anapita kukasodza
Yoh. 21:4-14—Yesu ataukitsidwa, anaonekela kwa Petulo komanso kwa ophunzila ena
Yoh. 21:15-19—Yesu anathandiza Petulo kuona zimene afunika kuika patsogolo (“Yesu anafunsa Simoni Petulo”, “Kodi Umandikonda Ine Kuposa Izi?”, “kacitatu” nwtsty mfundo zounikila pa Yoh. 21:15, 17)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Yoh. 20:17—Kodi mawu amene Yesu anauza Mariya Mmagadala atanthauza ciani? (“Usandikangamile” nwtsty mfundo younikila)
Yoh. 20:28—N’cifukwa ciani Tomasi anatomola Yesu kuti “Mbuyanga ndi Mulungu wanga”? (“Mbuyanga ndi Mulungu wanga” nwtsty mfundo younikila)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Yoh. 20:1-18
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Kubwelelako Koyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.
Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) bhs peji 79 mapa. 21-22. Itanilani munthuyo ku misonkhano.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (15 min.)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 42
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 45 na Pemphelo