LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 November tsa. 4
  • November 19-25

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • November 19-25
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 November tsa. 4

November 19-25

MACHITIDWE 4-5

  • Nyimbo 73 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Anapitiliza kulankhula Mawu a Mulungu Molimba Mtima”: (10 min.)

    • Mac. 4:5-13—Olo kuti Petulo na Yohane anali “osaphunzila ndiponso anthu wamba,” iwo sanaleke kuteteza cikhulupililo cawo kwa olamulila, na alembi (w08 9/1 peji 15, bokosi; w08 5/15 peji 30 pala. 6)

    • Mac. 4:18-20—Ngakhale kuti Petulo na Yohane anaopsezedwa, iwo sanaleke kulalikila

    • Mac. 4:23-31—Akhristu a m’nthawi ya atumwi anadalila mzimu woyela wa Yehova kuti akhale olimba mtima (it-1 peji 128 pala. 3)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Mac. 4:11—Kodi Yesu ni “mwala wofunika kwambili wapakona” m’lingalilo lanji? (it-1 peji 514 pala. 4)

    • Mac. 5:1—N’cifukwa ciani Hananiya na Safira anagulitsa munda wawo? (w13 3/15 peji 15 pala. 4)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mac. 5:27-42

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Mwininyumba akambe zimene anthu a m’gawo lanu amakamba posafuna kuwalalikila.

  • Kubwelelako Koyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Mwininyumba akukuuzani kuti si Mkhristu.

  • Vidiyo ya Kubwelelako Kaciŵili: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 82 na Pemphelo

  • “Mapindu a pa Dziko Lonse a Ulaliki wa pa Kasitandi”: (15 min.) Nkhani yokambilana yokambiwa na woyang’anila utumiki. Tambitsani vidiyoyi. Ngati mpingo wanu umaseŵenzetsa thebulo kapena kasitandi pocita ulaliki wapoyela, onetsani zimenezo kwa omvela. Fotokozani makonzedwe a mpingo wanu. Ngati nthawi ilipo, fotokozani cocitika cabwino kapena citani citsanzo ca zimene zinacitikazo. Fotokozani zimene ofalitsa angacite kuti azicitako ulaliki umenewu.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 43 pala. 8-18

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 64 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani