LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 December tsa. 4
  • December 17-23

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • December 17-23
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 December tsa. 4

December 17-23

MACHITIDWE 15-16

  • Nyimbo 96 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Cigamulo Cozikidwa pa Mawu a Mulungu”: (10 min.)

    • Mac. 15:1, 2—Nkhani ya mdulidwe inakula moti ikanagaŵanitsa mpingo woyambilila wacikhristu (bt mapeji 102-103 pala. 8)

    • Mac. 15:13-20—Cigamulo ca bungwe lolamulila cinali cozikidwa pa Malemba (w12 1/15 peji 5 mapa. 6-7)

    • Mac. 15:28, 29; 16:4, 5—Cigamulo ca bungwe lolamulila cinalimbitsa mipingo (bt peji 123 pala. 18)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Mac. 16:6-9—Kodi nkhaniyi itiphunzitsa ciani za kuwonjezela utumiki wathu? (w12 1/15 peji 10 pala. 8)

    • Mac. 16:37—Kodi mtumwi Paulo anaseŵenzetsa bwanji unzika wake waciroma kuti akwanilitse nchito yolalikila uthenga wabwino? (““ndife Aroma” nwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mac. 16:25-40

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Yankhani pa zimene anthu a m’gawo lanu amakamba posafuna kuwalalikila.

  • Kubwelelako Koyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. Chulani na kukambilana vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (koma musaitambitse)

  • Vidiyo ya Kubwelelako Kaciŵili: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 74

  • “Muziimba Mosangalala Nyimbo Zotamanda Yehova”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Ana Atamanda Yehova m’Nyimbo. Potsiliza mbaliyi, pemphani onse kuti aimilile na kuimbila pamodzi nyimbo ya pa vidiyo, namba 084 ya mutu wakuti Kudzipeleka na Mtima Wonse.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 46

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 102 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani