LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 January tsa. 6
  • January 28–February 3

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • January 28–February 3
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 January tsa. 6

January 28–February 3

MACHITIDWE 27-28

  • Nyimbo 129 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Paulo Apita ku Roma”: (10 min.)

    • Mac. 27:23, 24—Mngelo anauza Paulo kuti iye pamodzi na onse amene anali nawo pa ulendowu adzapulumuka ku cimphepo ca m’kuntho (bt peji 208 pala. 15)

    • Mac. 28:1, 2—Ngalawa imene Paulo anakwela inasweka pa cisumbu cochedwa melita (bt peji 209 pala. 18; peji 210 pala. 21)

    • Mac. 28:16, 17—Paulo anafika bwino ku Roma (bt peji 213 pala. 10)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Mac. 27:9—Kodi “kusala kudya kwa tsiku la mwambo wophimba macimo” kunali kutanthauza ciani?(“kusala kudya kwa tsiku la mwambo wophimba macimo” nwtsty mfundo younikila)

    • Mac. 28:11—N’ciani cocititsa cidwi na cizindikilo ca ngalawa? (“Ana Amapasa a Zeu” nwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mac. 27:1-12 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Kubwelelako Kaciŵili: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Kubwelelako Kaciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 2)

  • Phunzilo la Baibo: (5 min. olo kucepelapo) lv mape. 139-141 mapa. 16-17 (th phunzilo 3)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 103

  • “Paulo Anayamika Mulungu Ndipo Analimba Mtima”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti “Citsulo Cimanola Citsulo Cinzake”—Kambali Kake. Limbikitsani onse kuti akatambe vidiyo yonse.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 52

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 93 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani