LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 March tsa. 4
  • March 18-24

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 18-24
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 March tsa. 4

March 18-24

1 AKORINTO 1-3

  • Nyimbo 127 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba. (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Ndimwe Munthu Wakuthupi Kapena Wauzimu?”: (10 min.)

    • [Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Akorinto Woyamba.]

    • 1 Akor. 2:14—Kodi kukhala munthu wakuthupi kumatanthauza ciani? (w18.02 19 ¶4-5)

    • 1 Akor. 2:15, 16—Kodi kukhala “munthu wauzimu” kumatanthauza ciani? (w18.02 19 ¶6; 22 ¶15)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • 1 Akor. 1:20—Kodi Mulungu anapanga bwanji “nzelu za dzikoli kukhala zopusa”? (it-2 1193 ¶1)

    • 1 Akor. 2:3-5—Kodi citsanzo ca Paulo cingatithandize bwanji? (w08 7/15 27 ¶6)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) 1 Akor. 1:1-17 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi..

  • Ulendo Wobwelelako Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 3)

  • Ulendo Wobwelelako Woyamba: (4 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo, ndiyeno gaŵilani buku la Zimene Baibulo Ingatiphunzitse. (th phunzilo 11)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 18

  • “Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kulemba Bwino Makalata”: (8 min.) Kukambilana.

  • Kampeni Yomemeza Anthu ku Cikumbutso Idzayamba pa Ciŵelu, March 23: (7 min.) Nkhani yokambidwa na woyang’anila utumiki. Gaŵilani aliyense m’gulu kapepa koitanila anthu ku cikumbutso na kukambilana zimene zilimo. Tambitsani na kukambilana vidiyo ya ulaliki wacitsanzo. Fotokozani makonzedwe a mpingo wanu a mmene gawo lidzafoledwela.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 59

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 51 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani