May 6-12
2 AKORINTO 4-6
Nyimbo 128 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Sitikubwelela M’mbuyo”: (10 min.)
2 Akor. 4:16—Yehova amatipatsa mphamvu “tsiku ndi tsiku” (w04 8/15 25 ¶16-17)
2 Akor. 4:17—Mavuto amene timakumana nawo ni “akanthawi ndipo ndi opepuka” (it-1 724-725)
2 Akor. 4:18—Tifunika kusumika maganizo athu pa madalitso a Ufumu a kutsogolo
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
2 Akor. 4:7—Kodi mawu akuti “cuma cimeneci m’zonyamulila zoumbidwa ndi dothi” atanthauza ciani? (w12 2/1 28-29)
2 Akor. 6:13—Kodi tingatsatile bwanji malangizo akuti ‘tifutukule mitima yathu’? (w09 11/15 21 ¶7)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) 2 Akor. 4:1-15 (th phunzilo 12)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa: (10 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti, Kuŵelenga Bwino. Ndiyeno kambilanani phunzilo 5 m’bulosha ya Kuphunzitsa.
Nkhani: (5 min. olo kucepelapo) w04 7/1 30-31—Mutu: Kodi Mkhristu Wobatizika Ayenela Kukhala pa Cibwenzi na Wofalitsa Wosabatizika? (th phunzilo 7)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Kucita Zonse Zimene Ningathe: (8 min.) Tambitsani vidiyoyi. Ndiyeno funsani omvela mafunso aya: Kodi pamene M’bale Foster anali mnyamata wamphamvu, anacita bwanji zonse zotheka kuti atumikile Yehova? Kodi zinthu zinasintha bwanji mu umoyo wake? Ngakhale kuti umoyo wake unasintha, kodi m’baleyu amacitabe bwanji zonse zotheka potumikila Yehova? Nanga muphunzilapo zinthu zotani kwa iye?
Zofunikila za Mpingo: (7 min.)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 65
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 65 na Pemphelo