May 13-19
2 AKORINTO 7-10
Nyimbo 109 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Utumiki Wathu Wothandiza Pakacitika Tsoka: (10 min.)
2 Akor. 8:1-3—Akhristu a ku Makedoniya, anapeleka “ngakhale zoposa” pa zimene akanatha, kuti athandize abale awo a ku Yudeya (w98 11/1 25 ¶1; kr 209 ¶1)
2 Akor. 8:4—Kuthandiza Akhristu ovutika ni mbali ya ‘utumiki wathu wothandiza’ anthu (kr 209-210 ¶4-6)
2 Akor. 9:7—“Mulungu amakonda munthu wopeleka mokondwela” (kr 196 ¶10)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
2 Akor. 9:15—Kodi “mphatso [ya Mulungu] yaulele imene sitingathe n’komwe kuifotokoza” n’ciani? (w16.01 12 ¶2)
2 Akor. 10:17—Kodi ‘kudzitamanda mwa Yehova’ kutanthauza ciani? (g99 7/8 26-27)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) 2 Akor. 7:1-12 (th phunzilo 12)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 1)
Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Mukayamba makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso, kopani cidwi cake. (th phunzilo 2)
Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Mukayamba makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso, kopani cidwi cake. (th phunzilo 4)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Mmene Utumiki Wathu Wothandiza Patacitika Tsoka Wapindulitsila Abale Athu ku Caribbean”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti, Kuonetsa Cikondi M’zocita—Nchito Yothandiza Patacitika Tsoka ku Zisumbu
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 66
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 94 na Pemphelo