LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 June tsa. 3
  • June 10-16

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • June 10-16
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 June tsa. 3

June 10-16

AEFESO 1-3

  • Nyimbo 112 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Colinga ca Dongosolo la Mulungu”: (10 min.)

    • [Tambitsani vidiyo yakuti, Mfundo Zokhudza Buku la Aefeso.]

    • Aef. 1:8, 9—Ufumu wa Mesiya ni mbali ya “cinsinsi copatulika” (it-2 837 ¶4)

    • Aef. 1:10—Yehova akugwilizanitsa onse a m’banja lake (w12 7/15 27-28 ¶3-4)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Aef. 3:13—Kodi masautso a Paulo, anatanthauza “ulemelelo” kwa Akhristu a ku Efeso m’lingalilo lanji? (w13 2/15 28 ¶15)

    • Aef. 3:19—Kodi timacidziŵa motani “cikondi ca Khristu”? (cl 299 ¶21)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Aef. 1:1-14 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 1)

  • Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Mukayamba makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso, kopani cidwi cake. (th phunzilo 3)

  • Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo, ndiyeno gaŵilani cofalitsa ca mu Thuboksi Yathu. (th phunzilo 9)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 95

  • “Pangitsani Phunzilo Lanu Laumwini Kukhala Lopindulitsa”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Pitilizani “Kugwila Mwamphamvu” mwa Kucita Phunzilo Laumwini Lopindulitsa.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 70

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 144 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani