July 15-21
2 ATESALONIKA 1-3
Nyimbo 67 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Wosamvela Malamulo Aonekela”: (10 min.)
[Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la 2 Atesalonika.]
2 Ates. 2:6-8—“Wosamvela malamuloyo,” amene alipo kale, adzaonekela (it-1 972-973)
2 Ates. 2:9-12—Anthu amene amasoceletsedwa na “wosamvela malamulo,” adzaweluzidwa (it-2 245 ¶7)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
2 Ates. 1:7, 8—Kodi Yesu pamodzi na angelo adzaonekela motani “m’moto walawi-lawi”? (it-1 834 ¶5)
2 Ates. 2:2—Kodi Paulo anatanthauza ciani pamene anakamba mawu akuti “mawu ouzilidwa”? (it-1 1206 ¶4)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) 2 Ates. 1:1-12 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Ulendo Wobwelelako Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 6)
Ulendo Wobwelelako Woyamba: (4 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo, ndiyeno gaŵilani buku yakuti Zimene Baibulo Ingatiphunzitse. (th phunzilo 12)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Kodi Munaleka Kusangalala na Ulaliki?: (15 min.) Tambitsani vidiyo yakuti Wonjezelani Cangu pa Utumiki Wanu—Motani?
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 75
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 111 na Pemphelo