July 22-28
1 TIMOTEYO 1-3
Nyimbo 103 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kalamilani Nchito Yabwino”: (10 min.)
[Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la 1 Timoteyo.]
1 Tim. 3:1—Abale akulimbikitsidwa kuti afunika kukalamila kuti akhale oyang’anila (w16.08 21 ¶3)
1 Tim. 3:13—Abale amene amatumikila bwino amalandila madalitso (km 9/78 4 ¶7)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
1 Tim. 1:4—N’cifukwa ciani Paulo anacenjeza Timoteyo za kukumbana mibadwo ya makolo? (it-1 914-915)
1 Tim. 1:17—N’cifukwa ciani ni Yehova cabe amene angachedwe “Mfumu yamuyaya”? (cl 12 ¶15)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) 1 Tim. 2:1-15 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 2)
Phunzilo la Baibo: (5 min. olo kucepelapo) lvs 47-48 ¶6-7 (th phunzilo 6)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Anchito Acicepele Alemekeza Yehova ku Warwick: (6 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi. Ndiyeno kambilanani mafunso aya:
Kodi abale na alongo acicepele anathandiza bwanji pomanga Beteli ku Warwick? Nanga anapindula bwanji?
Kodi abale na alongo acicepele mu mpingo ali na mwayi wanji woonetsa kuti amalemekeza Yehova?
“Kodi Mungaphunzile Ciani kwa Iwo?”: (9 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Muzilemekeza Aciyambakale.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 76
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 115 na Pemphelo