LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 August tsa. 2
  • August 5-11

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • August 5-11
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 August tsa. 2

August 5-11

2 TIMOTEYO 1-4

  • Nyimbo 150 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mulungu Sanatipatse Mzimu Wamantha”: (10 min.)

    • [Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la 2 Timoteyo.]

    • 2 Tim. 1:7—Khalani ‘oganiza bwino’ pokumana na mayeselo (w09 5/15 15 ¶9)

    • 2 Tim. 1:8—Musamacite manyazi na uthenga wabwino (w03 3/1 9 ¶7)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • 2 Tim. 2:3, 4—Kodi tingapewe bwanji kudziloŵetsa kwambili mu “zamalonda zimene anthu wamba amacita”? (w17.07 10 ¶13)

    • 2 Tim. 2:23—Kodi “mafunso opusa ndi opanda nzelu” tingawakane bwanji? (w14 7/15 14 ¶10)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) 2 Tim. 1:1-18 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa: (10 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Mafanizo Ophunzitsadi Kanthu, ndiyeno kambilanani phunzilo 8 m’bulosha ya Kuphunzitsa.

  • Nkhani: (5 min. olo kucepelapo) w14 7/15 13 ¶3-7—Mutu: Kodi Anthu a Yehova Amaleka Bwanji “Kucita Zosalungama”? (th phunzilo 7)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 85

  • “Muziyanjana na Anthu Okonda Yehova”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Phunzilani Kupewa Makhalidwe Oipa.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 78

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 126 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani