LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 August tsa. 4
  • August 12-18

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • August 12-18
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 August tsa. 4

August 12-18

TITO 1–FILIMONI

  • Nyimbo 99 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kuika Akulu”: (10 min.)

    • [Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Tito.]

    • Tito 1:5-9—Oyang’anila madela amaika munthu kukhala mkulu ngati wakwanilitsa ziyenelezo za m’Malemba (w14 11/15 28-29)

    • [Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Filimoni.]

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Tito 1:12—N’cifukwa ciani mawu a pa vesiyi sacilikiza kusankhana mitundu? (w89 5/15 31 ¶5)

    • Filim. 15, 16—N’cifukwa ciani Paulo sanapemphe Filimoni kuti amasule Onesimo? (w08 10/15 31 ¶4)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Tito 3:1-15 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 3)

  • Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Mukayamba makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso, loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 12)

  • Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani kakhadi kongenela pa webusaiti. (th phunzilo 11)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 84

  • “Acinyamata—Khalani ‘Odzipeleka pa Nchito Zabwino’”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti, Acicepele Olemekeza Yehova.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 79

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 127 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani