August 19-25
AHEBERI 1-3
Nyimbo 35 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kondani Cilungamo, Danani Nako Kusamvela Malamulo”: (10 min.)
[Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Aheberi.]
Aheb. 1:8—Yesu akulamulila na “ndodo ya cilungamo” (w14 2/1 10 ¶8)
Aheb. 1:9—Yesu amakonda cilungamo, komanso amadana na kusamvela malamulo (w14 2/1 9 ¶7)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Aheb. 1:3—Kodi Yesu wakhala akuonetsa bwanji cifanizilo ca Atate ŵake ndendende? (it-1 1185 ¶1)
Aheb. 1:10-12—N’cifukwa ciani mtumwi Paulo anaseŵenzetsa Salimo 102:25-27 pokamba za Yesu Khristu? (it-1 1063 ¶7)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Aheb. 1:1-14 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Ulendo Wobwelelako Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 4)
Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Gaŵilani mwininyumba kapepa koitanila anthu ku misonkhano, ndiyeno chulani za vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? (Koma musaitambitse) (th phunzilo 11)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (15 min.)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 80
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 101 na Pemphelo