September 30–October 6
YAKOBO 1-2
Nyimbo 122 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Zimene Zimabweletsa Macimo na Imfa”: (10 min.)
[Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo zokhudza buku la Yakobo.]
Yak. 1:14—Kuganizila zolakwika kungatipangitse kuyamba kulaka-laka zinthu zoipa (g17.4 14)
Yak. 1:15—Nthawi zambili kulaka-laka zinthu zoipa kumatsogolela ku ucimo na imfa (g17.4 14)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Yak. 1:17—N’cifukwa ciani Yehova amachedwa “Atate wa zounikila zonse zakuthambo”? (it-2 253-254)
Yak. 2:8—Kodi “lamulo lacifumu” n’ciani? (it-2 222 ¶4)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Yak. 2:10-26 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Wobwelelako Wacitatu: (3 min. olo kucepelapo) Sankhani mwekha lemba. Ndipo itanilani mwininyumba ku misonkhano. (th phunzilo 3)
Ulendo Wobwelelako Wacitatu: (4 min. olo kucepelapo) Sankhani mwekha lemba. Ndiyeno gaŵilani cofalitsa cophunzitsila Baibo. (th phunzilo 12)
Phunzilo la Baibo: (5 min. olo kucepelapo) bhs 30 ¶4-5 (th phunzilo 13)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Pitilizani Kuganizila Zimenezi”: (8 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Muzipewa Zinthu Zimene Zingakulepheletseni Kukhala Wokhulupilika —Zosangulutsa Zoipa.
Makolo—Thandizani Ana Anu Kupewa Kutumizilana Zolaula: (7 min.) Nkhani yokambidwa na mkulu yozikidwa mu Galamukani! ya November 2013 mapeji 4-5.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 86 ¶1-7
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 130 na Pemphelo