October 21-27
1 PETULO 3-5
Nyimbo 14 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mapeto a Zinthu Zonse Ayandikila”: (10 min.)
1 Pet. 4:7—“Khalani oganiza bwino, ndipo khalani maso kuti musanyalanyaze kupemphela (w13 11/1 7 ¶1)
1 Pet. 4:8—“Khalani okondana kwambili” (w99 4/15 22 ¶3)
1 Pet. 4:9—“Muzicelezana popanda kudandaula” (w18.03 14-15 ¶2-3)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
1 Pet. 3:19, 20—Kodi ni liti pamene Yesu analalikila “mizimu imene inali m’ndende,” ndipo anacita bwanji zimenezi? (w13 6/15 23)
1 Pet. 4:6—Kodi “uthenga wabwino unalengezedwa” kwa “akufa” ati? (w08 11/15 21 ¶8)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) 1 Pet. 3:8-22 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Ulendo Wobwelelako Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 6)
Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno, chulani na kukambilana vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (koma musaitambitse) (th phunzilo 8)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Khalidwe Loyela na Ulemu Waukulu Zimakopa Mtima”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Yehova Amatithandiza pa Mavuto.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 88 ¶1-11
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 61 na Pemphelo