LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 November tsa. 2
  • November 4-10

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • November 4-10
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 November tsa. 2

November 4-10

1 YOHANE 1-5

  • Nyimbo 122 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Musamakonde Dziko Kapena Zinthu za M’dziko”: (10 min.)

    • [Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la 1 Yohane.]

    • 1 Yoh. 2:15, 16—‘Ciliconse ca m’dziko . .  sicicokela kwa Atate, koma kudziko’ (w05 1/1 10 ¶13)

    • 1 Yoh. 2:17—Dziko likupita limodzi na cilako-lako cake (w13 8/1 27 ¶18)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • 1 Yoh. 2:7, 8—Kodi lamulo limene Yohane anakamba pa mavesiwa linakhala bwanji lakale ndiponso latsopano? (w13 9/1 10 ¶14)

    • 1 Yoh. 5:16, 17—Kodi chimo “lobweletsa imfa” n’lotani? (it-1 862 ¶5)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) 1 Yoh. 1:1–2:6 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa: (10 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Kukamba Mwaumoyo. Ndiyeno, kambilanani phunzilo 11 m’bulosha ya Kuphunzitsa.

  • Nkhani: (5 min. olo kucepelapo) w04 10/1 29—Mutu: Kodi Yohane anatanthauzanji pa 1 Yohane 4:18, pamene anakamba kuti “cikondi cimene cili cokwanila cimathetsa mantha”? (th phunzilo 7)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 132

  • “Pewani Kutengela Maganizo a Dziko Pokonzekela Cikwati”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Maukwati Amene Amalemekeza Yehova.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu. 89

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 118 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani