LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 December tsa. 2
  • December 2-8

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • December 2-8
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 December tsa. 2

December 2-8

CHIVUMBULUTSO 7-9

  • Nyimbo 63 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Khamu Lalikulu Losaŵelengeka Likudalitsidwa na Yehova”: (10 min.)

    • Chiv. 7:9—“Khamu lalikulu” liimilila pamaso pa mpando wacifumu wa Yehova (it-1 997 ¶1)

    • Chiv. 7:14—Khamu lalikulu lidzapulumuka pa “cisautso cacikulu” (it-2 1127 ¶4)

    • Chiv. 7:15-17—Khamu lalikulu lidzalandila madalitso m’tsogolo pa dziko lapansi (it-1 996-997)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Chiv. 7:1—Kodi ‘angelo anayi oimilila m’makona anayi a dziko lapansi’ na “mphepo zinayi” aimila ciani? (re 115 ¶4)

    • Chiv. 9:11—Kodi “mngelo wa phompho” n’ndani?(it-1 12)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Chiv. 7:1-12 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa: (10 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Mzimu Waubwenzi na Cifundo, ndiyeno kambilanani phunzilo 12 m’bulosha ya Kuphunzitsa.

  • Nkhani: (5 min. olo kucepelapo) w16.01 25-26 ¶12-16—Mutu: N’cifukwa ciani sitifunika kudandaula na kuculuka kwa ciŵelengelo ca anthu amene akhala akudya zophiphilitsa za pa Cikumbutso m’zaka zaposacedwapa? (th phunzilo 6)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 93

  • Zofunikila za Mpingo: (8 min.))

  • Zimene Gulu Likukwanilitsa: (7 min.) Tambitsani vidiyo ya December yakuti Zimene Gulu Likukwanilitsa.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 93

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 27 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani