LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 December tsa. 3
  • December 9-15

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • December 9-15
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 December tsa. 3

December 9-15

CHIVUMBULUTSO 10-12

  • Nyimbo 26 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “‘Mboni Ziŵili’ Zinaphedwa, Kenako Zinakhalanso na Moyo”: (10 min.)

    • Chiv. 11:3—‘Mboni ziŵili’ zinalosela kwa masiku 1,260 (w14 11/15 30)

    • Chiv. 11:7—Mbonizo zinaphedwa na “cilombo”

    • Chiv. 11:11—‘Mboni ziŵili’ zimenezi zinakhalanso na moyo pambuyo pa masiku atatu na hafu

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Chiv. 10:9, 10—Kodi uthenga umene Yohane analandila unali woŵaŵa komanso ‘wonzuna’ motani? (it-2 880-881)

    • Chiv. 12:1-5—Kodi mawu a pa mavesiwa anakwanilitsidwa bwanji? (it-2 187 ¶7-9)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Chiv. 10:1-11 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 6)

  • Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo pocita ulaliki wa mwayi wogwilizana na gawo lanu. (th phunzilo 3)

  • Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani cofalitsa ca mu Thuboksi yathu. (th phunzilo 9)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 148

  • “Dzikolo ‘Linameza Mtsinje’”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Abale ku Korea Atulutsidwa M’ndende.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 94

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 47 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani