February 3-9
GENESIS 12-14
Nyimbo 14 na Pemphelo
Mawu Oyamba (1 min.)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Cipangano Cimene Cimakukhudzani”: (10 min.)
Gen. 12:1, 2—Yehova analonjeza kuti adzamudalitsa Abulamu (Abulahamu) (it-1 522 ¶4)
Gen. 12:3—“Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso cifukwa ca [Abulahamu].” (w89 7/1 3 ¶4)
Gen. 13:14-17—Yehova analongoza Abulahamu dziko limene mbadwa zake zidzakhalamo (it-2 213 ¶3)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)
Gen. 13:8, 9—Tingatengele bwanji citsanzo ca Abulahamu pothetsa mikangano? (w16.05 5 ¶12)
Gen. 14:18-20—Kodi Levi anapeleka bwanji “zakhumi” kupitila mwa Abulahamu? (Aheb. 7:4-10; it-2 683 ¶1)
Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova Mulungu, ulaliki, kapena mbali ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Gen. 12:1-20 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa: (10 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Kumveketsa Bwino Mfundo Zazikulu, ndiyeno kambilanani phunzilo 14 m’bulosha ya Kuphunzitsa.
Nkhani: (5 min. olo kucepelapo) w12 1/1 8—Mutu: N’ciani Cinapangitsa Sara Kukhala Wamtengo Wapatali? (th phunzilo 14)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Kodi Mungaphunzile Ciani mu Nyimbo Zopekedwa Koyamba?”: (10 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo ya nyimbo yopekedwa koyamba yakuti Dziko Latsopano Ili Pafupi Kwambili.
Zofunikila za Mpingo: (5 min.)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 102
Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)
Nyimbo 15 na Pemphelo