February 10-16
GENESIS 15-17
Nyimbo 39 na Pemphelo
Mawu Oyamba (1 min.)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Anasintha Dzina la Abulamu na Sarai —Cifukwa?”: (10 min.)
Gen. 17:1—Olo kuti anali wopanda ungwilo, Abulamu anaonetsa kuti anali wopanda colakwa (it-1 817)
Gen. 17:3-5—Dzina la Abulamu linasinthidwa kukhala Abulahamu (it-1 31 ¶1)
Gen. 17:15, 16—Dzina la Sarai linasinthidwa kukhala Sara (w09 2/1 13)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)
Gen. 15:13, 14—Ni liti pamene zaka 400 za masautso zinayamba na kutha? (it-1 460-461)
Gen. 15:16—Kodi mbadwa za Abulahamu zinabwelela bwanji ku Kanani mu “m’badwo wacinayi”? (it-1 778 ¶4)
Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova Mulungu, ulaliki, kapena mbali ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Gen. 15:1-21 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi. Kenako funsani omvetsela mafunso otsatilawa: Kodi wofalitsa waseŵenzetsa bwanji mafunso mwaluso? Kodi waseŵenzetsa motani fanizo pophunzitsa?
Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Mukayamba makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso, loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 3)
Ulendo Woyamba: (5 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani bulosha ya Uthenga Wabwino, na kuyambitsa Phunzilo la Baibo m’phunzilo 3. (th phunzilo 6)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Mmene Mwamuna na Mkazi Wake Angalimbitsile Cikwati Cawo”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Zimene Mungacite Kuti Mulimbitse Cikwati Canu.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 103
Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)
Nyimbo 92 na Pemphelo