LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 March tsa. 2
  • March 2-8

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 2-8
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 March tsa. 2

March 2-8

GENESIS 22-23

  • Nyimbo 89 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mulungu . . . Anamuyesa Abulahamu”: (10 min.)

    • Gen. 22:1, 2—Mulungu anauza Abulahamu kuti apeleke nsembe Isaki mwana wake wokondedwa (w12 1/1 23 ¶4-6)

    • Gen. 22:9-12—Yehova anauza Abulahamu kuti asamuphe Isaki

    • Gen. 22:15-18—Yehova analonjeza Abulahamu kuti adzamudalitsa cifukwa cokhala womvela (w12 10/15 23 ¶6)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)

    • Gen. 22:5—N’cifukwa ciani Abulahamu anauza anyamata ake kuti iye na Isaki adzaŵapeza ngakhale kuti Abulahamuyo anali kudziŵa kuti akukam’peleka nsembe Isaki? (w16.02 11 ¶13)

    • Gen. 22:12—Kodi lembali lionetsa bwanji kuti Yehova amacita kusankha kuseŵenzetsa nzelu zake zodziŵilatu za kutsogolo? (it-1 853 ¶5-6)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova Mulungu, ulaliki, kapena mbali ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Gen. 22:1-18 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa (10 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Kukamba Motsimikiza, ndiyeno kambilanani phunzilo 15 m’bulosha ya Kuphunzitsa.

  • Nkhani: (5 min. olo kucepelapo) it-1 604 ¶5—Mutu: N’cifukwa Ciani Abulahamu Anaonedwa Kukhala Wolungama Khristu Asanapeleke Moyo Wake? (th phunzilo 7)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 4

  • Kumvela Kumatiteteza: (15 min.) Tambitsani vidiyo yakuti Msonkhano wa Pacaka wa 2017—Nkhani na Lemba la Caka ca 2018—Kambali Kake.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 106

  • Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)

  • Nyimbo 16 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani