LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 March tsa. 5
  • March 23-29

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 23-29
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 March tsa. 5

March 23-29

GENESIS 27-28

  • Nyimbo 10 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yakobo Analandila Madalitso Omuyenelela”: (10 min.)

    • Gen. 27:6-10—Rabeka anathandiza Yakobo kulandila madalitso a mwana wake woyamba kubadwa (w04 4/15 11 ¶4-5)

    • Gen. 27:18, 19—Yakobo anapangitsa atate ŵake kuganiza kuti iye ni Esau (w07 10/1 31 ¶2-3)

    • Gen. 27:27-29—Isaki anapatsa Yakobo madalitso a mwana woyamba kubadwa (it-1 341 ¶6)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)

    • Gen. 27:46–28:2—Ni phunzilo lanji limene okwatilana angatengepo pa citsanzo ca Isaki na Rabeka? (w06 4/15 6 ¶3-4)

    • Gen. 28:12, 13—Kodi maloto a Yakobo okhudza “makwelelo” anatanthauza ciani? (w04 1/15 28 ¶6)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova Mulungu, ulaliki, kapena mbali ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Gen. 27:1-23 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (5 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi, ndiyeno funsani omvetsela mafunso otsatilawa: Kodi wofalitsa waonetsa bwanji kuti anali kumvetsela mwininyumba pamene anali kufotokoza maganizo ake? Kodi wofalitsa waseŵenzetsa bwanji mwaluso zida za mu Thuboksi yathu?

  • Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 6)

  • Phunzilo la Baibo: (5 min. olo kucepelapo) jl phunzilo 17 (th phunzilo 11)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 34

  • Zofunikila za Mpingo: (15 min.)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 109

  • Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)

  • Nyimbo 28 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani