LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 April tsa. 4
  • Yakobo na Labani Acita Pangano la Mtendele

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yakobo na Labani Acita Pangano la Mtendele
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Nkhani Zofanana
  • Yakobo Ayenda Ku Harana
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
  • Mudzakhala “Ufumu wa Ansembe”
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2014
  • Yehova Ananenelatu za Pangano Latsopano
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 April tsa. 4

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 31

Yakobo na Labani Acita Pangano la Mtendele

31:44-53

N’cifukwa ciani Yakobo na Labani anaunjika mulu wa miyala?

  • Mulu wa miyalawo unali umboni kwa odutsa wakuti iwo anacita pangano la mtendele

  • Unali kuwakumbutsa kuti Yehova anali kuyang’ana kuti aone ngati iwo akusunga pangano lawo la mtendele

Zithunzi: 1. M’Nyumba ya Ufumu, alongo aŵili akuyang’anana mwaukali. Cakumbuyo abale na alongo akuceza mokondwela. 2. Alongo amodzi-modzi akhala pamodzi m’lesitilanti inayake, akumwa tiyi ndipo akuceza mokondwela. Pa tebulo pali mphatso na Baibo.

Masiku ano, Yehova amafuna kuti tizikhala mwamtendele ndi abale na alongo athu. Kodi kucita zinthu zitatu zotsatilazi kungatithandize bwanji kukhazikitsa mtendele kapena kuubwezeletsa?

  • Kukambilana.—Mat. 5:23, 24

  • Kukhululukilana na mtima wonse.—Akol. 3:13

  • Kukhala woleza mtima.—Aroma 12:21

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani