LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 April tsa. 6
  • April 27–May 3

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • April 27–May 3
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 April tsa. 6

April 27–May 3

GENESIS 34-35

  • Nyimbo 28 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Zotulukapo Zoopsa za Mayanjano Oipa”: (10 min.)

    • Gen. 34:1—Mobweleza-bweleza Dina anali kupita kukaceza na ana aakazi acikanani (w97 2/1 30 ¶4)

    • Gen. 34:2—Sekemu anagwilila Dina (lvs 124 ¶14)

    • Gen. 34:7, 25—Simiyoni na Levi anapha Sekemu pamodzi na mwamuna aliyense wa mumzindawo (w09 9/1 21 ¶1-2)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)

    • Gen. 35:8—Kodi Debora anali ndani? Nanga tingaphunzile ciani kwa iye? (it-1 600 ¶4)

    • Gen. 35:22-26—Tidziŵa bwanji kuti kukhala pa mzele wa makolo a Mesiya sikunadalile kukhala woyamba kubadwa? (w17.12 14)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova Mulungu, ulaliki, kapena mbali ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Gen. 34:1-19 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (5 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi. Ndiyeno funsani omvetsela mafunso otsatilawa: Kodi Elise wayesetsa bwanji kum’fika pamtima mwininyumba? Kodi tingayambitse bwanji phunzilo la Baibo m’buku la Zimene Baibulo Ingatiphunzitse?

  • Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 13)

  • Phunzilo la Baibo: (5 min. olo kucepelapo) fg phunzilo 4 ¶6-7 (th phunzilo 14)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 40

  • “Cotsani Milungu Yacilendo”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti “Tsutsani Mdyelekezi”.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 112

  • Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)

  • Nyimbo 143 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani