LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 June tsa. 2
  • June 1-7

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • June 1-7
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 June tsa. 2

June 1-7

GENESIS 44-45

  • Nyimbo 130 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yosefe Anakhululukila Abale Ake”: (10 min.)

    • Gen. 44:1, 2—Yosefe anayesa abale ake kuti aone ngati anasintha (w15 5/1 14-15)

    • Gen. 44:33, 34—Yuda anacondelela Yosefe kuti amasule Benjamini

    • Gen. 45:4, 5—Yosefe anatengela citsanzo ca Yehova pokhululukila abale ake

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)

    • Gen. 44:13—Kodi kung’amba covala kunali kutanthauza ciani? (it-2 813)

    • Gen. 45:5-8—N’ciani cingatithandize kupilila zinthu zopanda cilungamo? (w04 8/15 15 ¶15)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova Mulungu, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Gen. 45:1-15 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa: (10 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Nkhani Yophunzitsadi Kanthu Omvela, ndiyeno kambilanani phunzilo 18, m’bulosha ya Kuphunzitsa.

  • Nkhani: (5 min. olo kucepelapo) w06 2/1 31—Mutu: Kodi Yosefe pogwilitsila nchito kapu yapadela yasiliva anawombezadi maula, monga mmene zingaonekele pa Genesis 44:5, 15? (th phunzilo 18)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 58

  • Zofunikila za Mpingo: (10 min.)

  • Zimene Gulu Likukwanilitsa: (5 min.) Tambitsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Likukwanilitsa ya June.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 117

  • Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)

  • Nyimbo 19 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani