June 8-14
GENESIS 46-47
Nyimbo 86 na Pemphelo
Mawu Oyamba (1 min.)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Thandizo la Cakudya pa Nthawi ya Njala”: (10 min.)
Gen. 47:13—M’dziko la Iguputo komanso la Kanani munagwa njala yaikulu (w87 5/1 15 ¶2)
Gen. 47:16, 19, 20—Aiguputo anafunika kudzimana zinthu zina kuti akhalebe na moyo
Gen. 47:23-25—Khama n’lofunika kuti tipindule na cakudya cauzimu ca mwana alilenji cimene tili naco masiku ano (kr 234-235 ¶11-12)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)
Gen. 46:4—Kodi Yehova anatanthauza ciani pamene anauza Yosefe kuti ni amene ‘adzatseka maso’ a Yakobo? (it-1 220 ¶1)
Gen. 46:26, 27—Kodi ni anthu angati a m’nyumba ya Yakobo amene analoŵa mu Iguputo? (nwtsty mfundo younikila pa Mac. 7:14)
Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova Mulungu, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Gen. 47:1-17 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi, ndiyeno funsani omvetsela mafunso aya: Kodi wofalitsa uja waseŵenzetsa bwanji mafunso mwaluso? Kodi wamveketsa bwanji mfundo ya palemba?
Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo, ndiyeno gaŵilani cofalitsa ca mu Thuboksi yathu. (th phunzilo 3)
Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo, ndiyeno gaŵilani buku lakuti Zimene Baibulo Ingatiphunzitse, ndipo yambitsani phunzilo la Baibo m’mutu 9. (th phunzilo 14)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Musaleke Kuŵelenga na Kusunga Zikumbutso za Yehova: (15 min.) Tambitsani vidiyo yakuti, Muziyamikila Zikumbutso za Yehova. Limbikitsani onse kuti apitilize kuŵelenga Mawu a Mulungu komanso kupindula na cakudya cauzimu cimene tili naco.—Yes. 25:6; 55:1; 65:13; Mat. 24:45.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 118
Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)
Nyimbo 109 na Pemphelo