July 6-12
EKSODO 6-7
Nyimbo 150 na Pemphelo
Mawu Oyamba (1 min.)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Tsopano Uona Zimene Ndicite kwa Farao”: (10 min.)
Eks. 6:1—Mose anali kudzacitila umboni “dzanja lamphamvu” la Yehova
Eks. 6:6, 7—Aisiraeli anali kudzapulumutsidwa (it-2 436 ¶3)
Eks. 7:4, 5—Farao na Aiguputo anali kudzadziŵa kuti Yehova ndani (it-2 436 ¶1-2)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)
Eks. 6:3—Yehova sanadzidziŵikitse kwa Abulahamu, Isaki na Yakobo, m’lingalilo lotani? (it-1 78 ¶3-4)
Eks. 7:1—Kodi Mose anali monga “Mulungu” kwa Farao m’njila iti? Nanga Aroni anakhala “mneneli” wa Mose m’njila yotani? (it-2 435 ¶5)
Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova Mulungu, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Eks. 6:1-15 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa: (10 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Yesetsani Kuwafika pa Mtima Omvela, ndiyeno kambilanani phunzilo 19, m’bulosha ya Kuphunzitsa.
Nkhani: (5 min. olo kucepelapo) w15 1/15 9 ¶6-7—Mutu: Muziyamika Yehova Tsiku Lililonse. (th phunzilo 19)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (15 min.)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 122
Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)
Nyimbo 42 na Pemphelo