August 3-9
EKSODO 13-14
Nyimbo 148 na Pemphelo
Mawu Oyamba (1 min.)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Cilimikani ndi Kuona Cipulumutso ca Yehova”: (10 min.)
Eks. 14:13, 14—Mose anali na cikhulupililo cakuti Yehova adzapulumutsa Aisiraeli (w13 2/1 4)
Eks. 14:21, 22—Yehova anawapulumutsa mozizwitsa (w18.09 26 ¶13)
Eks. 14:26-28—Yehova anawononga Farao na gulu lake la asilikali (w09 3/15 7 ¶2-3)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)
Eks. 13:17—Kodi Yehova anaonetsa bwanji kuwaganizila Aisiraeli powatulutsa mu Iguputo? (it-1 1117)
Eks. 14:2—Kodi Nyanja Yofiila inagawidwa pa malo ati kuti Aisiraeli awoloke? (it-1 782 ¶2-3)
Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Eks. 13:1-20 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa: (10 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Mawu Otsiliza Ogwila Mtima, ndiyeno kambilanani phunzilo 20 m’bulosha ya Kuphunzitsa.
Nkhani: (5 min. olo kucepelapo) w07 12/15 18-20 ¶13-16—Mutu: Kodi Tiphunzilapo Ciani Tikaona Mmene Yehova Anapulumutsila Aisiraeli pa Nyanja Yofiila? (th phunzilo 13)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Cilimikani Pamene Mapeto Ayandikila”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Zocitika Zam’tsogolo Zimene Zidzafuna Kulimba Mtima —Kambali Kake.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 126
Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)
Nyimbo 128 na Pemphelo