LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 August tsa. 8
  • August 31–September 6

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • August 31–September 6
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 August tsa. 8

August 31–September 6

EKSODO 21-22

  • Nyimbo 141 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzionetsa kuti Mumaona Moyo Mmene Yehova Amauonela”: (10 min.)

    • Eks. 21:20—Yehova amaletsa kupha munthu (it-1 271)

    • Eks. 21:22, 23—Yehova amaona moyo wa mwana wosabadwa kukhala wamtengo wapatali (lvs 95 ¶16)

    • Eks. 21:28, 29—Yehova amafuna kuti tizitsatila malangizo acitetezo (w10 4/15 29 ¶4)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)

    • Eks. 21:5, 6—Malinga na mavesiwa, kodi tikadzipatulila kwa Yehova timapindula motani? (w10 1/15 4 ¶4-5)

    • Eks. 21:14—Kodi mfundo ya palembali tingaifotokoze motani? (it-1 1143)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Eks. 21:1-21 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno itanilani munthuyo ku misonkhano. (th phunzilo 2)

  • Ulendo Wobwelelako: (4 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno chulani na kukambilana vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? (koma musaitambitse) (th phunzilo 20)

  • Nkhani: (5 min. olo kucepelapo) w09 4/1 31—Mutu: Yehova—Atate wa Ana Amasiye. (th phunzilo 19)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 60

  • Muziona Moyo Mmene Mulungu Amauonela: (10 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi. Ndiyeno funsani omvetsela: Kodi pa nthawi imene mayi ali na pakati pangabuke zovuta zotani? Kodi lemba la Ekisodo 21:22, 23 ili na mfundo yanji pankhani ya kucotsa mimba? N’cifukwa ciani cikhulupililo na kulimba mtima n’zofunika kuti tipange cosankha cokondweletsa Yehova? Kodi ciyembekezo ca ciukililo cimatitonthoza bwanji?

  • Mmene Kudzipatulila Kumatipindulitsila: (5 min.) Nkhani yozikidwa mu Nsanja Yolonda ya January 15, 2010, peji 4, mapalagilafu 4-7. Limbikitsani ophunzila Baibo kuti apite patsogolo kuti akadzipatulile na kubatizika.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 130

  • Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)

  • Nyimbo 15 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani