LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 November tsa. 3
  • November 9-15

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • November 9-15
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 November tsa. 3

November 9-15

LEVITIKO 1-3

  • Nyimbo 20 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Colinga ca Nsembe”: (10 min.)

    • [Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Levitiko.]

    • Lev. 1:3; 2:1, 12—Colinga ca nsembe zopseleza na nsembe zambewu (it-2 525; 528 ¶4)

    • Lev. 3:1—Colinga ca nsembe zaciyanjano (it-2 526 ¶1)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)

    • Lev. 2:13—N’cifukwa ciani nsembe iliyonse anali kuithila mcele? (Ezek. 43:24; w04 5/15 22 ¶2)

    • Lev. 3:17—N’cifukwa ciani Aisiraeli anali kuletsedwa kudya mafuta a nyama? Nanga tiphunzilapo ciani pamenepa? (it-1 813; w04 5/15 22 ¶3)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Lev. 1:1-17 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako: (5 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo imeneyi. Nthawi iliyonse vidiyo ikaima, na imwe iimitseni na kufunsa omvetsela mafunso amene aonekela pa sikilini.

  • Ulendo Wobwelelako: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 2)

  • Ulendo Wobwelelako: (5 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani cofalitsa ca mu Thuboksi Yathu. (th phunzilo 11)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 53

  • “Mphamvu ya ‘Tumakobili Tuŵili Twatung’ono’”: (15 min.) Nkhani yokambilana yokambidwa na mkulu. Tambitsani vidiyo yakuti ‘Kupeleka Mphatso kwa Yehova.’ Ŵelengani kalata yocokela ku nthambi yoyamikila zopeleka zimene yalandila m’caka ca utumiki capita.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min. olo kucepelapo) jy peji 317

  • Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)

  • Nyimbo 120 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani