LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 December tsa. 6
  • December 28, 2020–January 3, 2021

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • December 28, 2020–January 3, 2021
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 December tsa. 6

December 28–January 3

LEVITIKO 16-17

  • Nyimbo 41 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Zimene Tingaphunzile pa Zocitika za pa Tsiku la Mwambo Wophimba Macimo”: (10 min.)

    • Lev. 16:12—Mophiphilitsa, mkulu wa ansembe anali kuonekela pamaso pa Yehova (w19.11 21 ¶4)

    • Lev. 16:13—Mkulu wa ansembe anali kufukiza zofukiza kwa Yehova (w19.11 21 ¶5)

    • Lev. 16:14, 15—Kenako mkulu wa ansembe anali kupeleka nsembe kuti aphimbe macimo a ansembe ndi a anthu (w19.11 21 ¶6)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)

    • Lev. 16:10—Kodi mbuzi ya Azazeli inacitila cithunzi nsembe ya Yesu m’njila ziti? (it-1 226 ¶3)

    • Lev. 17:10, 11—N’cifukwa ciani timakana kuikidwa magazi? (w14 11/15 10 ¶10)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Lev. 16:1-17 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Mukayamba makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso, loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 3)

  • Ulendo Wobwelelako: (4 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Kenako gaŵilani buku lophunzitsila Baibo. (th phunzilo 4)

  • Phunzilo la Baibo: (5 min. olo kucepelapo) fg phunzilo 1 ¶1-2 (th phunzilo 14)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 70

  • “Kodi Mungakonde Kufunsila Kuti Mukaloŵe Sukulu ya Alengezi a Ufumu?”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Amishonale—Anchito Okolola.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min. olo kucepelapo) lfb phunzilo 12

  • Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)

  • Nyimbo 35 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani