LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsa. 8
  • January 25-31

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • January 25-31
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 January tsa. 8

January 25-31

LEVITIKO 24-25

  • Nyimbo 144 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Caka ca Ufulu Komanso Ufulu Wam’tsogolo”: (Mph. 10.)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 10.)

    • Lev. 24:20—Kodi mawu a Mulungu amalimbikitsa kubwezela? (w09 9/1 22 ¶4)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4.) Lev. 24:1-23 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba (Mph. 3.) Mukayamba makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki, koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 16)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4.) Yambani na makambilano acitsanzo. Gaŵilani mwininyumba kapepa koitanila kumisonkhano. Ndiyeno chulani na kukambilana vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? (koma musaitambitse) (th phunzilo 11)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5.) fg phunzilo 12 ¶6-7 (th phunzilo 14)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 139

  • Zofunikila za Mpingo (Mph. 5.)

  • “Tidzapeza Ufulu M’tsogolo mwa Thandizo la Mulungu na Khristu”: (Mph. 10.) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Pamene Mphepo ya Mkuntho Ikuyandikila, Pitilizani Kuyang’anitsitsa Yesu!—Madalitso a Ufumu a Mtsogolo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30.) lfb phunzilo 17

  • Mawu Othela (Mph. 3.)

  • Nyimbo 12 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani