LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsa. 10
  • February 1-7

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • February 1-7
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 January tsa. 10

February 1-7

LEVITIKO 26–27

  • Nyimbo 89 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Zimene Tingacite Kuti Tilandile Madalitso a Yehova”: (Mph. 10.)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 10.)

    • Lev. 26:16—Kodi Yehova analanga Aisiraeli na mlili m’lingalilo lotani? (it-2 617)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4.) Lev. 26:18-33 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3.) Yambani na makambilano acitsanzo. Gaŵilani kakhadi kongenela pa webusaiti yathu. (th phunzilo 11)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4.) Yambani na makambilano acitsanzo. Gaŵilani cofalitsa ca mu Thuboksi yathu. (th phunzilo 6)

  • Nkhani: (Mph. 5.) w09 8/1 30—Mutu: Kodi Mulungu Amafuna Kuti Nizipeleka Ndalama Zingati? (th phunzilo 16)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 40

  • “Sankhani Kutumikila Yehova”: (Mph. 15.) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Zimene Mungacite Kuti Muyenelele Ubatizo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30.) lfb phunzilo 18, 19

  • Mawu Othela (Mph. 3.)

  • Nyimbo 2 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani