LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsa. 2
  • March 1-7

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 1-7
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 March tsa. 2

March 1-7

NUMERI 7-8

  • Nyimbo 4 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Zimene Tingaphunzile pa Dongosolo la Msasa wa Aisiraeli”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Num. 8:17—Kodi Yehova anali kuwaona bwanji ana aamuna oyamba kubadwa mu Isiraeli? (it-1 835)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Num. 7:1-17 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Kuitanila Anthu ku Cikumbutso: (Mph. 2) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 11)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Citani ulendo wobwelelako kwa munthu amene anaonetsa cidwi ndipo analandila ciitanilo ca ku Cikumbutso. (th phunzilo 6)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Itanilani ku Cikumbutso munthu amene munali kuphunzila naye Baibo kale. (th phunzilo 12)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Itanilani ku Cikumbutso wacibale amene munamulalikilako kumbuyoku. (th phunzilo 17)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 54

  • Zimene Gulu Likukwanilitsa: (Mph. 5) Onetsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Likukwanilitsa ya March.

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 10)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 25

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 92 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani