March 22-28
NUMERI 13-14
Nyimbo 118 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mmene Cikhulupililo Cimatithandizila Kukhala Olimba Mtima”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Num. 13:27—Kodi azondi anakamba ciani cimene cikanalimbitsa cikhulupililo ca Aisiraeli mwa Yehova? (Lev. 20:24; it-1 740)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Num. 13:1-20 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Nkhani: (Mph. 5) w15 9/15 14-16 ¶8-12—Mutu: Mafunso Amene Angatithandize Kufufuza Cikhulupililo Cathu. (th phunzilo 14)
“Wonjezelani Cimwemwe Canu mu Ulaliki—Funsani Mafunso”: (Mph. 10) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Pezani Cimwemwe pa Nchito Yopanga Ophunzila—Nolani Maluso Anu—Kufunsa Mafunso.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Cimene Akhristu Oona Afunikila Kukhala Olimba Mtima—Polalikila: (Mph. 8) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Ndiyeno funsani omvetsela mafunso awa: Kodi mlongo Kitty Kelly anali na vuto lotani? N’ciani cinamuthandiza kukhala wolimba mtima? Kodi anapeza mapindu otani cifukwa cokhala wolimba mtima?
Cimene Akhristu Oona Afunikila Kukhala Olimba Mtima—Kuti Asamatengeko Mbali M’zandale: (Mph. 7) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Ndiyeno funsani mafunso awa: Kodi m’bale Ayenge Nsilu anakumana na mavuto otani? Kodi anacita zotani zimene zinam’thandiza kukhalabe wolimba mtima? Nanga anamvetsetsa ciani cimene cinam’thandiza kudalila Yehova?
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 28
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 121 na Pemphelo