LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsa. 10
  • April 5-11

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • April 5-11
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 March tsa. 10

April 5-11

NUMERI 17-19

  • Nyimbo 80 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Ine Ndine . . . Colowa Cako”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Num. 18:19, mawu amunsi—Kodi mawu akuti “pangano la mcele” atanthauza ciani? (g02 6/8 14 ¶2)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Num. 18:1-13 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Wobwelelako: Yesu—Mat. 20:28. Nthawi iliyonse vidiyo ikaima, na imwe iimitseni na kufunsa omvetsela mafunso amene aonekela pasikilini.

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani cofalitsa ca mu Thuboksi yathu. (th phunzilo 6)

  • Nkhani: (Mph. 5) w18.01 18 ¶4-6—Mutu: N’cifukwa Ciani Timapeleka Cuma Cathu kwa Yehova? (th phunzilo 20)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 117

  • Zofunikila za Mpingo (Mph. 15)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30.) lfb phunzilo 30

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 8 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani